Esitere 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga onse a mʼzigawo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito za mfumu ankathandiza Ayudawo chifukwa ankaopa Moredikayi.
3 Akalonga onse a mʼzigawo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito za mfumu ankathandiza Ayudawo chifukwa ankaopa Moredikayi.