Esitere 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moredikayi anali ndi mphamvu zambiri+ mʼnyumba ya mfumu ndipo anatchuka mʼzigawo zonse chifukwa anapitiriza kukhala ndi mphamvu.
4 Moredikayi anali ndi mphamvu zambiri+ mʼnyumba ya mfumu ndipo anatchuka mʼzigawo zonse chifukwa anapitiriza kukhala ndi mphamvu.