Esitere 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsikuli mfumu inauzidwa chiwerengero cha anthu amene anaphedwa kunyumba ya mfumu ya ku Susani* yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.
11 Pa tsikuli mfumu inauzidwa chiwerengero cha anthu amene anaphedwa kunyumba ya mfumu ya ku Susani* yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.