-
Esitere 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno mfumu inauza Mfumukazi Esitere kuti: “Kunyumba ya mfumu ya ku Susani* yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri, Ayuda apha amuna 500 komanso ana 10 a Hamani. Ndiye kuli bwanji mʼzigawo zina zonse za mfumu?+ Panopa ukufuna kupempha chiyani? Ndikupatsa. Pali zinanso zimene ukufuna kupempha? Zimene ukufuna zichitika.”
-