Esitere 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Esitere anayankha kuti: “Ngati mungavomereze mfumu,+ bwanji mawa Ayuda amene ali ku Susani* achitenso zimene lamulo laleroli likunena?+ Ndikupemphanso kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+
13 Esitere anayankha kuti: “Ngati mungavomereze mfumu,+ bwanji mawa Ayuda amene ali ku Susani* achitenso zimene lamulo laleroli likunena?+ Ndikupemphanso kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+