Esitere 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho mfumu inalamula kuti achite zimenezo ndipo lamulo linaperekedwa ku Susani.* Komanso ana aamuna 10 a Hamani anapachikidwa.
14 Choncho mfumu inalamula kuti achite zimenezo ndipo lamulo linaperekedwa ku Susani.* Komanso ana aamuna 10 a Hamani anapachikidwa.