Esitere 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani* anasonkhananso pa tsiku la 14 la mwezi wa Adara,+ ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanatenge zinthu zawo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Nsanja ya Olonda,3/1/2006, tsa. 113/15/1986, tsa. 28
15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani* anasonkhananso pa tsiku la 14 la mwezi wa Adara,+ ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanatenge zinthu zawo.