Esitere 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nawonso Ayuda ena onse amene anali mʼzigawo za mfumu anasonkhana kuti adziteteze.+ Ndipo anapha adani awo+ okwana 75,000 koma sanatenge zinthu zawo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Nsanja ya Olonda,3/1/2006, tsa. 113/15/1986, tsa. 28
16 Nawonso Ayuda ena onse amene anali mʼzigawo za mfumu anasonkhana kuti adziteteze.+ Ndipo anapha adani awo+ okwana 75,000 koma sanatenge zinthu zawo.