-
Esitere 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Limeneli linali tsiku la 13 la mwezi wa Adara. Ndiyeno pa tsiku la 14 anapuma nʼkuchita phwando ndipo anasangalala kwambiri.
-