Esitere 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ayuda amene anali ku Susani* anasonkhana pa tsiku la 13+ ndi la 14+ la mweziwo. Iwo anapuma pa tsiku la 15 ndipo anachita phwando komanso chikondwerero.
18 Ayuda amene anali ku Susani* anasonkhana pa tsiku la 13+ ndi la 14+ la mweziwo. Iwo anapuma pa tsiku la 15 ndipo anachita phwando komanso chikondwerero.