Esitere 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nʼchifukwa chake Ayuda akumidzi amene ankakhala mʼmadera akutali ndi mzinda, anasankha kuti tsiku la 14 la mwezi wa Adara likhale tsiku lachikondwerero, lochita phwando, losangalala+ ndiponso lotumizirana chakudya.+
19 Nʼchifukwa chake Ayuda akumidzi amene ankakhala mʼmadera akutali ndi mzinda, anasankha kuti tsiku la 14 la mwezi wa Adara likhale tsiku lachikondwerero, lochita phwando, losangalala+ ndiponso lotumizirana chakudya.+