Esitere 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Moredikayi+ analemba zimene zinachitikazi nʼkutumiza makalata kwa Ayuda onse amene anali mʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero, zakutali ndiponso zapafupi.
20 Ndiyeno Moredikayi+ analemba zimene zinachitikazi nʼkutumiza makalata kwa Ayuda onse amene anali mʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero, zakutali ndiponso zapafupi.