-
Esitere 9:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Anawauza zimenezi chifukwa masiku amenewa Ayuda anasiya kuvutitsidwa ndi adani awo, komanso mʼmwezi umenewu chisoni chawo chinasintha nʼkukhala chikondwerero ndipo tsiku lolira+ linasintha nʼkukhala tsiku losangalala. Masiku amenewa ankayenera kukhala ochita phwando, kusangalala, kutumizirana chakudya ndiponso kupereka mphatso kwa anthu osauka.
-