-
Esitere 9:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndipo Ayuda anavomereza kuti apitiriza chikondwerero chimene anali atayamba kale komanso achita zimene Moredikayi anawalembera.
-