Esitere 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nʼchifukwa chake masiku amenewa anawapatsa dzina lakuti Purimu, kutengera dzina lakuti Puri.*+ Choncho chifukwa cha zonse zomwe zinalembedwa mʼkalatayi, zimene anaona pa nkhani imeneyi komanso zimene zinawachitikira,
26 Nʼchifukwa chake masiku amenewa anawapatsa dzina lakuti Purimu, kutengera dzina lakuti Puri.*+ Choncho chifukwa cha zonse zomwe zinalembedwa mʼkalatayi, zimene anaona pa nkhani imeneyi komanso zimene zinawachitikira,