Esitere 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ayudawo analonjeza kuti iwo, mbadwa zawo ndiponso anthu onse amene anakhala kumbali yawo,+ azichita chikondwerero masiku awiri amenewa komanso azichita zimene zinalembedwa zokhudza masikuwa pa nthawi yake chaka chilichonse.
27 Ayudawo analonjeza kuti iwo, mbadwa zawo ndiponso anthu onse amene anakhala kumbali yawo,+ azichita chikondwerero masiku awiri amenewa komanso azichita zimene zinalembedwa zokhudza masikuwa pa nthawi yake chaka chilichonse.