-
Esitere 9:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Mʼbadwo uliwonse uyenera kukumbukira masiku amenewa ndipo zizichitika mʼbanja lililonse, chigawo chilichonse ndiponso mzinda uliwonse. Ayuda sayenera kusiya kukumbukira masiku a Purimu ndipo mbadwa zawo siziyenera kusiya kukumbukira masiku amenewa.
-