-
Esitere 9:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno Mfumukazi Esitere, mwana wa Abihaili, komanso Moredikayi Myuda, analemba kalata yachiwiri ndi ulamuliro wonse, kutsimikizira za Purimu.
-