Esitere 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anatumiza makalata okhala ndi mawu amtendere ndiponso oona kwa Ayuda onse mʼzigawo 127+ zimene Ahasiwero ankalamulira.+
30 Kenako anatumiza makalata okhala ndi mawu amtendere ndiponso oona kwa Ayuda onse mʼzigawo 127+ zimene Ahasiwero ankalamulira.+