-
Esitere 9:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Anatumiza makalatawo kuti atsimikizire kuti azichita chikondwerero cha Purimu pa nthawi yake, mogwirizana ndi zimene Moredikayi Myuda ndi Mfumukazi Esitere anawalamulira kuti azichita.+ Komanso mogwirizana ndi zimene analonjeza kuti Ayudawo ndi mbadwa zawo azichita,+ kuphatikizapo kusala kudya+ komanso kupemphera mochonderera.+
-