Yobu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pambuyo pa zimenezi, linafika tsiku limene ana a Mulungu woona*+ anapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo Satana nayenso anapita kukaonekera pamaso pa Yehova.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, ptsa. 13-14
2 Pambuyo pa zimenezi, linafika tsiku limene ana a Mulungu woona*+ anapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo Satana nayenso anapita kukaonekera pamaso pa Yehova.+