Yobu 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Yehova anafunsa Satana kuti: “Kodi ukuchokera kuti iwe?” Satanayo anayankha Yehova kuti: “Ndimazungulira mʼdziko lapansi komanso kuyendayendamo.”+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 14
2 Kenako Yehova anafunsa Satana kuti: “Kodi ukuchokera kuti iwe?” Satanayo anayankha Yehova kuti: “Ndimazungulira mʼdziko lapansi komanso kuyendayendamo.”+