-
Yobu 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kapena ndi akalonga amene anali ndi golide,
Amene nyumba zawo zinadzaza ndi siliva.
-
15 Kapena ndi akalonga amene anali ndi golide,
Amene nyumba zawo zinadzaza ndi siliva.