Yobu 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nʼchifukwa chiyani anthu amene amafuna kufa, samafa?+ Iwo amakumba pansi pofunafuna imfa, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika.
21 Nʼchifukwa chiyani anthu amene amafuna kufa, samafa?+ Iwo amakumba pansi pofunafuna imfa, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika.