Yobu 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa mʼmalo moti ndidye chakudya ndimausa moyo,+Ndipo kubuula kwanga+ kumakhuthuka ngati madzi.
24 Chifukwa mʼmalo moti ndidye chakudya ndimausa moyo,+Ndipo kubuula kwanga+ kumakhuthuka ngati madzi.