Yobu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkango umabangula, ndipo mkango wamphamvu umamveka kulira,Komabe ngakhale mano a mikango yamphamvu,* amathyoka.
10 Mkango umabangula, ndipo mkango wamphamvu umamveka kulira,Komabe ngakhale mano a mikango yamphamvu,* amathyoka.