Yobu 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nanga kuli bwanji anthu amene amakhala mʼnyumba zadothi,Amene maziko awo ali mʼfumbi?+Amene amathudzulidwa mosavuta ngati kadziwotche. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Nsanja ya Olonda,2/15/2010, ptsa. 19-202/1/1994, tsa. 29
19 Nanga kuli bwanji anthu amene amakhala mʼnyumba zadothi,Amene maziko awo ali mʼfumbi?+Amene amathudzulidwa mosavuta ngati kadziwotche.