Yobu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale zimenezo, zikanatha kunditonthoza.Ndikanadumpha ndi chisangalalo ngakhale kuti ndikumva ululu wosaneneka,Chifukwa sindinakane mawu a Woyerayo.+
10 Ngakhale zimenezo, zikanatha kunditonthoza.Ndikanadumpha ndi chisangalalo ngakhale kuti ndikumva ululu wosaneneka,Chifukwa sindinakane mawu a Woyerayo.+