-
Yobu 6:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kodi ndanena kuti, ‘Ndipatseni kanthu,’
Kapena kodi ndapempha kuti mundiperekere mphatso kuchokera pa chuma chanu?
-