Yobu 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu akamanena zoona, sizipweteka.+ Koma kodi kudzudzula kwanu kuli ndi phindu lanji?+