Yobu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kodi moyo wa munthu padziko lapansi suli ngati ntchito yokakamiza?Ndipo kodi masiku ake sali ngati masiku a munthu waganyu?+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 14
7 “Kodi moyo wa munthu padziko lapansi suli ngati ntchito yokakamiza?Ndipo kodi masiku ake sali ngati masiku a munthu waganyu?+