Yobu 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi kapolo, iye amalakalaka mthunzi,Ndipo mofanana ndi munthu waganyu, iye amadikirira malipiro ake.+
2 Mofanana ndi kapolo, iye amalakalaka mthunzi,Ndipo mofanana ndi munthu waganyu, iye amadikirira malipiro ake.+