Yobu 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nʼchifukwa chiyani simukundikhululukira machimo anga,Nʼkunyalanyaza zolakwa zanga? Chifukwa posachedwapa ndigona mʼfumbi,+Ndipo mudzandifunafuna koma ine kudzakhala kulibe.”
21 Nʼchifukwa chiyani simukundikhululukira machimo anga,Nʼkunyalanyaza zolakwa zanga? Chifukwa posachedwapa ndigona mʼfumbi,+Ndipo mudzandifunafuna koma ine kudzakhala kulibe.”