Yobu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi ukhala ukulankhula chonchi mpaka liti?+ Mawu a mʼkamwa mwako ali ngati mphepo yamphamvu.