Yobu 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ngati ukanakhaladi woyera komanso ngati umachitadi zoyenera,+Iye akanakumvera*Ndipo akanakubwezeretsa mmene unalili poyamba.
6 Ndipo ngati ukanakhaladi woyera komanso ngati umachitadi zoyenera,+Iye akanakumvera*Ndipo akanakubwezeretsa mmene unalili poyamba.