Yobu 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nkhani yokhala ndi mphamvu, iye ndi wamphamvu kwambiri.+ Pa nkhani yochita zinthu mwachilungamo, iye amanena kuti: ‘Ndi ndani angandiimbe mlandu?’*
19 Pa nkhani yokhala ndi mphamvu, iye ndi wamphamvu kwambiri.+ Pa nkhani yochita zinthu mwachilungamo, iye amanena kuti: ‘Ndi ndani angandiimbe mlandu?’*