Yobu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi laperekedwa mʼmanja mwa anthu oipa.+Iye amaphimba maso a oweruza* a dzikolo. Ngati si iyeyo, ndiye ndi ndani?
24 Dziko lapansi laperekedwa mʼmanja mwa anthu oipa.+Iye amaphimba maso a oweruza* a dzikolo. Ngati si iyeyo, ndiye ndi ndani?