Yobu 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zili kutali kuposa kumwamba. Iwe sungathe kuzipeza. Nʼzozama kuposa Manda.* Ungadziwe chiyani iwe?