Yobu 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene zinthu zikuwayendera bwino amanyoza amene akumana ndi tsoka,Iwo amaganiza kuti limagwera anthu okhawo amene akukumana kale ndi mavuto.*
5 Amene zinthu zikuwayendera bwino amanyoza amene akumana ndi tsoka,Iwo amaganiza kuti limagwera anthu okhawo amene akukumana kale ndi mavuto.*