Yobu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Akaletsa mvula, chilichonse chimauma,+Akalola kuti ibwere, madzi amasefukira padziko lapansi.+