Yobu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amamasula zingwe zimene mafumu amangira anthu,+Ndipo amawamanga lamba mʼchiuno mwawo.