Yobu 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amaulula zinthu zozama zimene zili mumdima,+Ndipo amabweretsa kuwala mumdima wandiweyani.