Yobu 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Amachotsa nzeru za atsogoleri* a anthuwo,Ndipo amawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu mmene mulibe njira.+
24 Amachotsa nzeru za atsogoleri* a anthuwo,Ndipo amawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu mmene mulibe njira.+