Yobu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndikanakonda kulankhula ndi Wamphamvuyonse,Ndikulakalaka nditalankhula ndi Mulungu zokhudza mlandu wangawu.+
3 Ine ndikanakonda kulankhula ndi Wamphamvuyonse,Ndikulakalaka nditalankhula ndi Mulungu zokhudza mlandu wangawu.+