Yobu 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu anu anzeru* nʼchimodzimodzi ndi miyambi yosathandiza ngati phulusa.Mawu anu odziteteza ndi osathandiza ngati zishango zadothi.
12 Mawu anu anzeru* nʼchimodzimodzi ndi miyambi yosathandiza ngati phulusa.Mawu anu odziteteza ndi osathandiza ngati zishango zadothi.