Yobu 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale Mulungu atandipha, ndipitirizabe kumukhulupirira,+Ndisonyeza pamaso pake kuti ndine wosalakwa.*
15 Ngakhale Mulungu atandipha, ndipitirizabe kumukhulupirira,+Ndisonyeza pamaso pake kuti ndine wosalakwa.*