Yobu 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho munthu* amaola ngati chinthu chimene chayamba kuwonongeka,Ngati chovala chimene chadyedwa ndi njenjete.”*
28 Choncho munthu* amaola ngati chinthu chimene chayamba kuwonongeka,Ngati chovala chimene chadyedwa ndi njenjete.”*