Yobu 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nanga angakhulupirire bwanji munthu wonyansa amene amachita zoipa zokhazokha,+Munthu yemwe amamwa zinthu zopanda chilungamo ngati madzi? Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:16 Nsanja ya Olonda,2/15/2010, tsa. 20
16 Nanga angakhulupirire bwanji munthu wonyansa amene amachita zoipa zokhazokha,+Munthu yemwe amamwa zinthu zopanda chilungamo ngati madzi?