Yobu 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amamva phokoso lochititsa mantha mʼmakutu ake,+Pa nthawi yamtendere achifwamba amamuukira.