Yobu 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye sakhulupirira kuti adzatuluka mumdima,+Ndipo akudikira kuti aphedwe ndi lupanga.